[Intro: Montell Fish]
Talk to me, why don't you
Talk to me? Like you used to, you don't—
Talk to me, why don't you
Talk to me? Like you used to, you don't t
[Chorus: Ace Dirty]
Mwanakazi wakutowa (Horus Dem Baad)
Ndi mafuna ntakushowa
Chikondi Ndichosowa
Ndimangophakira Kabowa
Ndinagrower ndikublowa
Panopa tinalowa
[Post-Chorus: Krazie G]
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
[Verse 1: 60 Grxmz]
Ain't holdin' grudges my heart cold, don't wanna talk (fuck)
My life a movie smokin' doonie when I'm alone
Separated from the bullshit ndine dolo Mario Bro
Ndukatrapa parcel ku speed pa city mall (Mdubz nigga)
Now she sad mix amandiwonawona
Hella backshot tachita kugwira khoma
She's always like "baby ndimakusowa"
Sakuziwa wandikwana sister wake Ndishowa
Akufuna banja koma ine ndikufuna ndrama (Haa)
Akufuna mwana koma ine sindimupatsa
Wayipelekera ntafuna nditha kuthawa
Akufuna banja koma ine ndikufuna ndrama
[Chorus: Ace Dirty]
Mwanakazi wakutowa
Ndi mafuna ntakushowa
Chikondi Ndichosowa
Ndimangophakira Kabowa
Ndinagrower ndikublowa
Panopa tinalowa
[Post-Chorus: Krazie G]
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwе pakulowa mula
[Verse 2: Krazie G]
Tikulera mu restaurant, mwina ndidya Ka waiter
Ngati mbalе ya nsima kali ndima heat
Kabweletsa drip ndakapatsa tip, kafaka number pa recipt
I need to remember to call her later
Sizama love, no zimenezo you can die
Gangster satrapa heartbreak bola kuyika pipe
Dzina lake ndika Beat yup that's my type, type beat
Irish she's willing to ride me
Ding-Dong I'll get the door
Ine moneyo Ndi imene ndimakonda bro
Ndangosowa ngati Shinobiso
(Ndangosowa ngati Shinobiso)
[Chorus: Ace Dirty]
Mwanakazi wakutowa (Horus Dem Baad)
Ndi mafuna ntakushowa
Chikondi Ndichosowa
Ndimangophakira Kabowa
Ndinagrower ndikublowa
Panopa tinalowa
[Post-Chorus: Krazie G]
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
[Verse 3: Ace Dirty]
Ndili mkati chani? (Ha)
Ndili pa stage ndi zi utsi ngati magician
Ngini inasintha sindunamizani (wallahi)
Ma Bro's kuzablowa ngati Taliban (boom)
Mkazi iwe umati chani? (chani?)
Akusowa pogwira (ah, ah?)
Ine Ndi chi wave Utha kumila (splash)
Wafika Ndi chithako ati ukhoza kugwira (Mmh, hm)
She just wanna kick it nde titha kudhiwa
Achina Akila (aah)
[Chorus: Ace Dirty]
Mwanakazi wakutowa
Ndi mafuna ntakushowa
Chikondi Ndichosowa
Ndimangophakira Kabowa
Ndinagrower ndikublowa
Panopa tinalowa
[Post-Chorus: Krazie G]
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
Kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
[Outro: die Montell Fish]
Ayo Landie
We ain't got no time
Love me
Talk to me, why don't you
Talk to me? Like you used to, you don't—