Video Ndi Mmene Tiliri de Ace Tee 2025 Lyrics Lyrics

Escucha la música Lyrics más popular de Ace Tee y otros artistas en línea. Disfruta de las mejores canciones de 2025 en Musicas-Cristianas de música en línea. ¡Encuentra tu canción favorita y escúchala en cualquier momento y en cualquier lugar!

Video Ndi Mmene Tiliri » Ace Tee Letra

INICIOAce TeeNdi Mmene Tiliri

Ace Tee - Ndi Mmene Tiliri Lyrics


[Intro]
Classic
Ace-Tee on the beat

Whoa! Ine ndi Thossa, uyu ndi Yobezani
Big tings ah gwaan, roll out, mvetselani
Hip-op and dancehall, Thoss dem talk
Yoh, trap yuh ear, switch it on

[Verse 1: Huplex Thossa]
Mdalitso ndi wanga n'naukwelera phiri
N'napempha sauzande wandipatsa milli
Straight fram hustle chakhuminso ndi ichi
Osadabwa iwe, ndi m'mene tiliri
Yoh mi deh pan mi knees yea, Lord asante
Mtima unasweka, mwati muumate
Mi nuh fraid a none a dem, abwere sate
Timayenda ndi Tate
Nde ayi sitibisa, nah
Timapemphera, sitimakana
Ukationa tikupambana
Ndi m'mene tiliri, itsanana
Yoh Yobezani, ndi m'mene tiliri
Ambuye ali likiliki
Talking about God's tings zilibe tikiti
Go, go, go, go, go! Thoss dem
[Chorus]
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
[Pan Sunday inna Church]
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
[Sitimakhala ndi tense]
Ndi m'mene tiliri [yah, yah, yah, yah]
Ndi m'mene tiliri

[Verse 2: Yobezani]
I'm always vibing with my gang iwe taona
Spirited up ngati Sangoma
Sizamatama man kungoti ndinaborna
Space launched, dziko n'nadropper
Ndine wake, anandisintha lifestyle
Pondichitira chifundo ndili mu last mile
Now I live for Him mpake ndili agile
So I share hope, life yi ili fragile
Sindinkana, ndimam'tsata
Olo dziko lindide bwanji
Even atakhala Sattah n'kupanga
Zake zoti ndilidye banzi
Ndili ndi bread of life, za njala ndinachotsa
Ndinaiphula kale mpake ndima bosser
Mfunse Huplex, zinazi tinatosser
Sinditengeka 'cause I roll with the Most High
Let's go!
[Chorus]
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
[Pan Sunday inna Church]
Ndi m'mene tiliri
Ndi m'mene tiliri
[Sitimakhala ndi tense]
Ndi m'mene tiliri [yah, yah, yah, yah]
Ndi m'mene tiliri

[Outro]
So one mi jus buss dat
Fi mi Christ, big name, yuh jus know dat
Yoh Yobezani, tell dem, dem haffi know dat
Yea, yea, yea, yea, yea, yea, know dat
[Ace-Tee on the b...]
Yoh
Ndi m'mene tiliri aise, yea
Ndi m'mene tiliri
Iwe Madela
Ndi m'mene tiliri
Yea, yea, yea, yea, yea

Ndi Mmene Tiliri » Ace Tee Letras !!!
Esta sitio web no aloja ningún tipo de archivo audio o video© Musicas-Cristianas 2025 España | Chile - Argentina - México. Todos los derechos reservados.

Escuchar músicas enlinea gratis, 2025 Escuchar Música Online, Música en Línea 2025, Música en Línea Gratis, Escuchar Música Gratis, Música Online 2025, Escuchar Música

Música 2025, Música 2025 Online, Escuchar Música Gratis 2025, Músicas 2025 Gratis, Escuchas top, Música de Moda.