Video Ukununkhila de Achina Gattah Ase 2025 Lyrics Lyrics

Escucha la música Lyrics más popular de Achina Gattah Ase y otros artistas en línea. Disfruta de las mejores canciones de 2025 en Musicas-Cristianas de música en línea. ¡Encuentra tu canción favorita y escúchala en cualquier momento y en cualquier lugar!

Video Ukununkhila » Achina Gattah Ase Letra

INICIOAchina Gattah AseUkununkhila

Achina Gattah Ase - Ukununkhila Lyrics


[Intro : Crispy Malawi]
Yeah, um-
Hm, Hm, hm haa
Malawian
Yeah (Yeah)
Uh

[Chorus: Crispy Malawi]
How many times should I tell you, kuti ndimakufila
Ndungofuna tizichiller, Ukudripper ndikumila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila

[Verse 1: Crispy Malawi]
Ma guy mwandilira
Ngati muona chithako muzachigwira
Pa corner ndakupanilira, ndakumatilira
Sindikutripper yankha text, Phone yangothima
Bend down ngati ukulima
Kuthokaso Chilma, Ine ndikulima
Mmh mh Don't halla please, ndili high ndadya cannabis
Ati Spe "What is This?"
Ndagwira ass koma ndikufuna kiss
Been around never miss, ndika blower imakhala kiss
And ndimakhala busy nde usandipatse busy

[Chorus: Crispy Malawi]
Ndikuwuze Kangati kuti ndimakufila?
Ndungofuna tizichiller, Ukudripper ndikumila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila
Ndikuwuze Kangati kuti ndimakufila?
Ndungofuna tizichiller, Ukudripper ndikumila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila

[Verse 2: Crispy Malawi]
Uli fly sizofunika visa
Life is too short ngati Ndi Deezer [?]
Ndili busy, mindin' my bihness
Makape ali madzi tuwabatiza
We in the cut ngati scissors
Kavala bumshort ndima lipha
Ndango rocker Zima Yeezus
Tili Mangochi walkin' on water, ndungozifila ngati Jesus (Splash)
Feelin' my Ex, Chi body cha Bho tipange reverse

[Chorus: Crispy Malawi]
Ndikuwuze Kangati kuti ndimakufila?
Ndungofuna tizichiller, Ukudripper ndikumila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila

[Verse 3: Achina Gatta Ase, Hayze Engola & Crispy Malawi]
Yooh
Ndikuwuze Kangati kuti ndimakufila?
Sindinakuwuze dzina, chifukwa umandidziwa
Kaya uli Ndi mamuna, ndikungofuna kugwira
Zoti sukufuna (Mmh), sindikufuna kudziwa (Mmh)
Tivaye pawiri bwanji panotu Pali phokoso
Kuvaya pafupi kakungonunkhira ka Mafioso (Fe! Fe!)
Kuvaya ku date moti kazidya, busy ndima photo
Zonse Ndi chabe man Bola kugwidwa Ndi dolo
(Ndikuwuze Kangati?)
Kodi Iwe Jameela, tikukufuna Ndi angati?
Ndikungofuna kudziwa
Ine undimvetse ndikamati, Hayze akungochilla
Unakandifunsa ine ndinakati (Mmh hm) ndakumangilira (Mmh)
Tikumasula asavutike kumayankhula (Mmh)
Ndikudziwa Ali Ndi Freed mfana wopusher (Eeh)
Ndinamudziwa kale kale akumwa shooter
Usakhale ngati sukufuna mfana wophula
[Chorus: Crispy Malawi]
Ndikuwuze Kangati kuti ndimakufila?
Ndungofuna tizichiller, Ukudripper ndikumila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila

Ndikuwuze Kangati kuti ndimakufila?
Ndungofuna tizichiller, Ukudripper ndikumila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila
Fe! Fe! Fe! Fe! ukununkhila

Ukununkhila » Achina Gattah Ase Letras !!!
ANUNCIOS PUBLICITARIOS
Esta sitio web no aloja ningún tipo de archivo audio o video© Musicas-Cristianas 2025 España | Chile - Argentina - México. Todos los derechos reservados.

Escuchar músicas enlinea gratis, 2025 Escuchar Música Online, Música en Línea 2025, Música en Línea Gratis, Escuchar Música Gratis, Música Online 2025, Escuchar Música

Música 2025, Música 2025 Online, Escuchar Música Gratis 2025, Músicas 2025 Gratis, Escuchas top, Música de Moda.