[Intro]
Ayy, y'all, tiyeni
Tiyeni, tiyeni, tiyeni
[Hook]
Wadzuka bwanji neba, ndiwe wobhebha
Ufunika mamuna woti zake zikuyenda
Kamamuna kawo kakhoza kuyenda
Chabwino katsale 'fukwa akhoza kugenda
Heh, koma akangosuntha ndizibwera kwanu kudzafuntha
Ine ndi mfana wanjalatu, ndidzibwera kwanu kudzakhuta
[Chorus]
Cristina
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Iwe si nsima
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Iwe si nsima
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
[Verse]
Ndapeza muti athira mu Milo
Athira mu Milo
Bread mpakana ma peace four
Mpakana ma peace four
Mowa wanga andimwera
Ndapeza mowa wanga andimwera
Ndatsegula mu fridge mwanga ndi chi-confidence
Nyama yonse andidyera
Ndapeza muti athira mu Milo
Athira mu Milo
Bread mpakana ma peace four
Mpakana ma peace four
Mowa wanga andimwera
Ndapeza mowa wanga andimwera
Ndatsegula mu fridge mwanga ndi chi-confidence
Nyama yonse andidyera
[Hook]
Wadzuka bwanji neba, ndiwe wobhebha
Ufunika mamuna woti zake zikuyenda
Kamamuna kawo kakhoza kuyenda
Chabwino katsale 'fukwa akhoza kugenda
Heh, koma akangosuntha ndizibwera kwanu kudzafuntha
Ine ndi mfana wanjalatu, ndidzibwera kwanu kudzakhuta
[Chorus]
Cristina
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Iwe si nsima
(mphaka wachoka, makoswe atase)
Kutenga kudyera mu beamer
(mphaka wachoka, makoswe atase)
(mphaka wachoka, makoswe atase)
(mphaka wachoka, makoswe atase)
[Verse]
Ndapeza muti athira mu Milo
Athira mu Milo
Bread mpakana ma peace four
Mpakana ma peace four
Mowa wanga andimwera
Ndapeza mowa wanga andimwera
Ndatsegula mu fridge mwanga ndi chi-confidence
Nyama yonse andidyera
Ndapeza muti athira mu Milo
Athira mu Milo
Bread mpakana ma peace four
Mpakana ma peace four
Mowa wanga andimwera
Ndapeza mowa wanga andimwera
Ndatsegula mu fridge mwanga ndi chi-confidence
Nyama yonse andidyera
[Outro]
Mpaka, mpaka, mpaka, mpaka
Ayi, yah-yah-yah
Ayi, yah-yah-yah, yah-yah
Ayi, yah-yah, yah-yah-yah
Makoswe atase
Ayi, yah-yah-yah, eish
Tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni
Tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni, tiyeni
Ah-yeah-yeah